Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 77:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+

      Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+

  • Yesaya 40:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye adzasamalira* gulu la nkhosa zake ngati mʼbusa.+

      Ndi dzanja lake, adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa,

      Ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.

      Nkhosa zimene zikuyamwitsa adzazitsogolera mwachikondi.+

  • Yeremiya 31:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Inu mitundu ya anthu, imvani mawu a Yehova,

      Ndipo mulengeze mawuwo kuzilumba zakutali kuti:+

      “Amene anabalalitsa Aisiraeli ndi amene adzawasonkhanitse.

      Adzawayangʼanira ngati mmene mʼbusa amachitira ndi nkhosa zake.+

  • Ezekieli 34:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+

  • 1 Petulo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Poyamba munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa mʼbusa wanu+ ndi woyangʼanira miyoyo yanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena