Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamaso pa Yehova, chifukwa iye akubwera,*Iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi. Adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
13 Pamaso pa Yehova, chifukwa iye akubwera,*Iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi. Adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+