Salimo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+ Salimo 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova amadziwa mavuto amene anthu osalakwa akukumana nawo,*Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+
18 Yehova amadziwa mavuto amene anthu osalakwa akukumana nawo,*Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+