Salimo 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova amadziwa za moyo wa anthu osalakwa,+Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+