2 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo chikondi changa chokhulupirika sichidzachoka pa iye ngati mmene ndinachichotsera pa Sauli,+ amene ndinamʼchotsa pamaso pako. 1 Mafumu 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma fuko limodzi lipitiriza kukhala lake+ chifukwa cha mtumiki wanga Davide+ ndiponso chifukwa cha mzinda wa Yerusalemu umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli.+ 1 Mafumu 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwana wake ndidzamʼpatsa fuko limodzi kuti mtumiki wanga Davide apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mumzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha kuti ukhale ndi dzina langa.
15 Ndipo chikondi changa chokhulupirika sichidzachoka pa iye ngati mmene ndinachichotsera pa Sauli,+ amene ndinamʼchotsa pamaso pako.
32 Koma fuko limodzi lipitiriza kukhala lake+ chifukwa cha mtumiki wanga Davide+ ndiponso chifukwa cha mzinda wa Yerusalemu umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli.+
36 Mwana wake ndidzamʼpatsa fuko limodzi kuti mtumiki wanga Davide apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mumzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha kuti ukhale ndi dzina langa.