Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+ Salimo 76:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumawala kwambiri.*Ndinu waulemerero kuposa mapiri amene muli nyama zodya zinzake.
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+