Ekisodo 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukabwereketsa ndalama kwa munthu aliyense wosauka* pakati pa anthu anga, kwa munthu amene ali pafupi ndi inu, musakhale ngati munthu wopereka ngongole yakatapira kwa iye. Musamuuze kuti apereke chiwongoladzanja.+
25 Mukabwereketsa ndalama kwa munthu aliyense wosauka* pakati pa anthu anga, kwa munthu amene ali pafupi ndi inu, musakhale ngati munthu wopereka ngongole yakatapira kwa iye. Musamuuze kuti apereke chiwongoladzanja.+