Miyambo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Woipa amakodwa ndi zolakwa zake zomwe,Ndipo adzamangidwa ndi zingwe za tchimo lake lomwe.+ 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza Mulungu ndi wolungama, iye adzapereka chilango kwa amene amachititsa kuti muzizunzika.+