-
Chivumbulutso 6:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Atamatula chidindo cha 5, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo*+ ya anthu amene anaphedwa chifukwa cha mawu a Mulungu ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni.+ 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+
-