Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndidzatamanda Yehova amene wandipatsa malangizo.+

      Ngakhale usiku maganizo amkati mwa mtima wanga* amandiuza zoyenera kuchita.+

       8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+

      Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+

  • Miyambo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Palibe munthu amene angakhale wotetezeka chifukwa chochita zoipa,+

      Koma anthu olungama sadzazulidwa.

  • 2 Petulo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, nʼcholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha. Mukapitiriza kuchita zimenezi, simudzalephera ngakhale pangʼono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena