Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwatsala kanthawi kochepa, ndipo oipa sadzakhalaponso.+Udzayangʼana pamene ankakhala,Ndipo sadzapezekapo.+ Salimo 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anthu onse ochimwa adzawonongedwa.Mʼtsogolo, anthu oipa adzaphedwa.+
10 Kwatsala kanthawi kochepa, ndipo oipa sadzakhalaponso.+Udzayangʼana pamene ankakhala,Ndipo sadzapezekapo.+