Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.* Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala Mfumu!+ Dziko lapansi lisangalale.+ Zilumba zambiri zikondwere.+ Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+ Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinamva mawu amene ankamveka ngati mawu a khamu lalikulu, ngati mkokomo wa madzi ambiri komanso ngati mabingu amphamvu. Mawuwo anali akuti: “Tamandani Ya!*+ chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu!+
93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.*
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+
6 Kenako ndinamva mawu amene ankamveka ngati mawu a khamu lalikulu, ngati mkokomo wa madzi ambiri komanso ngati mabingu amphamvu. Mawuwo anali akuti: “Tamandani Ya!*+ chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu!+