-
Chivumbulutso 11:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndipo akulu 24+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu aja, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi ndipo analambira Mulungu. 17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+
-