Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Siyani kuchita zinthu zoipa ndipo muzichita zabwino.+

      Yesetsani kukhala mwamtendere ndi ena komanso kuulimbikitsa.+

  • Salimo 101:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.*

      Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+

      Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze.

  • Salimo 119:104
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 104 Ndimachita zinthu mozindikira chifukwa cha malamulo anu.+

      Nʼchifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+

  • Aroma 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chikondi chanu chisakhale chachiphamaso.+ Muzinyansidwa ndi zoipa+ nʼkumayesetsa kuchita zabwino.

  • Aheberi 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Unkakonda chilungamo ndipo unkadana ndi kusamvera malamulo. Nʼchifukwa chake Mulungu, Mulungu wako, anakudzoza+ ndi mafuta achisangalalo chachikulu kuposa mafumu anzako.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena