-
Danieli 3:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Kenako Nebukadinezara ananena kuti: “Atamandike Mulungu wa Shadireki, Misheki ndi Abedinego+ amene anatumiza mngelo wake nʼkudzapulumutsa atumiki ake. Atumiki akewo anamudalira ndipo sanamvere lamulo la mfumu, moti anali okonzeka kufa* mʼmalo motumikira kapena kulambira mulungu wina aliyense kupatulapo Mulungu wawo.+
-