Yohane 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sindikupempha kuti muwachotse mʼdziko, koma kuti muwateteze kwa woipayo.+ 1 Yohane 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tikudziwa kuti ndife anthu a Mulungu, koma dziko lonse lili mʼmanja mwa woipayo.*+