Nehemiya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinayankha mfumuyo kuti: “Mfumu mukhale ndi moyo wautali! Ndilekerenji kuoneka wachisoni pamene mzinda umene makolo anga anaikidwako uli bwinja ndipo mageti ake anatenthedwa ndi moto?”+ Salimo 137:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikakuiwala iwe Yerusalemu,Dzanja langa lamanja liiwale luso lake.+
3 Kenako ndinayankha mfumuyo kuti: “Mfumu mukhale ndi moyo wautali! Ndilekerenji kuoneka wachisoni pamene mzinda umene makolo anga anaikidwako uli bwinja ndipo mageti ake anatenthedwa ndi moto?”+