Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Inu amene mukundichotsa pakhomo la imfa,+

      Onani mmene anthu amene akudana nane akundizunzira,

      14 Kuti ndilengeze ntchito zanu zotamandika pamageti a mwana wamkazi wa Ziyoni,*+

      Komanso kuti ndisangalale chifukwa mwandipulumutsa.+

  • Salimo 22:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga.+

      Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+

  • Yesaya 51:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+

      Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+

      Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+

      Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,

      Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena