Genesis 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko lapansi linali lopanda chilichonse. Padzikoli panali madzi ambiri+ ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Mphamvu ya Mulungu+ inkayendayenda* pamwamba pa madziwo.+
2 Dziko lapansi linali lopanda chilichonse. Padzikoli panali madzi ambiri+ ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Mphamvu ya Mulungu+ inkayendayenda* pamwamba pa madziwo.+