Salimo 37:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,*+Uzimudalira ndipo iye adzakuthandiza.+ 6 Iye adzachititsa kuti kulungama kwako kuwale ngati mʼmawa,Ndipo chilungamo chako adzachichititsa kuti chiwale ngati dzuwa masana.
5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,*+Uzimudalira ndipo iye adzakuthandiza.+ 6 Iye adzachititsa kuti kulungama kwako kuwale ngati mʼmawa,Ndipo chilungamo chako adzachichititsa kuti chiwale ngati dzuwa masana.