Salimo 55:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuthandiza.+ Iye sadzalola kuti munthu wolungama agwe.*+ Miyambo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zochita zako zonse uzisiye mʼmanja mwa Yehova,*+Ndipo mapulani ako adzayenda bwino.
22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuthandiza.+ Iye sadzalola kuti munthu wolungama agwe.*+