Deuteronomo 32:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+ 10 Anamupeza mʼdziko lachipululu,+Mʼchipululu chopanda kanthu, molira zilombo.+ Anamuzungulira kuti amuteteze, anamusamalira,+Ndipo anamuteteza ngati mwana wa diso lake.+ Zekariya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+
9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+ 10 Anamupeza mʼdziko lachipululu,+Mʼchipululu chopanda kanthu, molira zilombo.+ Anamuzungulira kuti amuteteze, anamusamalira,+Ndipo anamuteteza ngati mwana wa diso lake.+
8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+