Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akupatse mphoto chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akulipire mokwanira* popeza wathawira mʼmapiko mwake kuti upeze chitetezo.”+ Salimo 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+ Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+
12 Yehova akupatse mphoto chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akulipire mokwanira* popeza wathawira mʼmapiko mwake kuti upeze chitetezo.”+
7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+ Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+