Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akupatse mphoto chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akulipire mokwanira* popeza wathawira mʼmapiko mwake kuti upeze chitetezo.”+ Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakuphimba ndi mapiko ake,Ndipo udzathawira pansi pa mapiko ake.*+ Kukhulupirika kwake+ kudzakhala chishango chako chachikulu+ komanso khoma lokuteteza.
12 Yehova akupatse mphoto chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akulipire mokwanira* popeza wathawira mʼmapiko mwake kuti upeze chitetezo.”+
4 Adzakuphimba ndi mapiko ake,Ndipo udzathawira pansi pa mapiko ake.*+ Kukhulupirika kwake+ kudzakhala chishango chako chachikulu+ komanso khoma lokuteteza.