Salimo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga.+Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+