Salimo 119:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Mtima wanga uzitsatira malangizo anu mosalakwitsa kanthu,+Kuti ndisachite manyazi.+