Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti mawu ake aulemerero+ amvekeNdipo adzapangitsa kuti dzanja lake+ limene likutsika ndi mkwiyo waukulu lionekere.+Dzanjalo lidzatsika ndi moto wowononga,+Mvula yamphamvu,+ mphezi komanso mvula yamatalala.+
30 Yehova adzapangitsa kuti mawu ake aulemerero+ amvekeNdipo adzapangitsa kuti dzanja lake+ limene likutsika ndi mkwiyo waukulu lionekere.+Dzanjalo lidzatsika ndi moto wowononga,+Mvula yamphamvu,+ mphezi komanso mvula yamatalala.+