Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+ Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Chifukwa wachita zinthu zodabwitsa.+ Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.*+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
98 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Chifukwa wachita zinthu zodabwitsa.+ Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.*+