Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo mundiletse kuchita zinthu modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+ Mukatero ndidzakhala wopanda chifukwa,+Komanso ndidzakhala wopanda mlandu wa machimo akuluakulu.* Salimo 37:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chilamulo cha Mulungu wake chili mumtima mwake.+Iye adzachitsatira nthawi zonse.+
13 Ndipo mundiletse kuchita zinthu modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+ Mukatero ndidzakhala wopanda chifukwa,+Komanso ndidzakhala wopanda mlandu wa machimo akuluakulu.*