15 Ngati kutumikira Yehova kukukunyansani, sankhani lero amene mukufuna kumʼtumikira,+ kaya milungu imene makolo anu ankaitumikira kutsidya lina la Mtsinje,+ kapena milungu ya Aamori amene mukukhala mʼdziko lawo.+ Koma ine ndi banja langa tizitumikira Yehova.”