Yoswa 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yoswa anauza anthuwo kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kale makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori, ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.+
2 Yoswa anauza anthuwo kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kale makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori, ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.+