Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 48:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti:

      “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,

      Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+

      Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+

  • Yohane 6:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zinalembedwa mʼMabuku a Aneneri kuti: ‘Onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.

  • Yakobo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena