Yesaya 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+ Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+
5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+