Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 15:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 ‘Zovala zanu zizikhala ndi ulusi kuti mukaziona muzikumbukira malamulo onse a Yehova ndi kuwasunga.+ Musamatsatire zilakolako za mitima yanu ndi maso anu, chifukwa nʼzimene zikukupangitsani kuti musakhale okhulupirika kwa ine.*+

  • Miyambo 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Maso ako aziyangʼana patsogolo.

      Inde, uziyangʼanitsitsa* zinthu zimene zili patsogolo pako.+

  • Miyambo 23:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Usadzitopetse pofuna kupeza chuma.+

      Leka kuchita zimenezi, mʼmalomwake uzisonyeza kuti ndiwe womvetsa zinthu.*

       5 Ukayangʼana pamene panali chumacho, umapeza kuti palibe,+

      Chifukwa ndithu chimamera mapiko ngati chiwombankhanga nʼkuulukira mʼmwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena