-
1 Timoteyo 6:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma anthu ofunitsitsa kulemera amakumana ndi mayesero ndiponso amakodwa mumsampha.+ Iwo amalakalaka zinthu zowapweteketsa komanso amachita zinthu mopanda nzeru. Zimenezi zimawawononga ndiponso kuwabweretsera mavuto.+ 10 Chifukwa kukonda ndalama kumayambitsa* zopweteka za mtundu uliwonse, ndipo chifukwa chotengeka ndi chikondi chimenechi, ena asiya chikhulupiriro ndipo adzibweretsera zopweteka zambiri pathupi lawo.+
-