Aroma 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa nʼcholinga choti tikhale ndi chiyembekezo.+
4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa nʼcholinga choti tikhale ndi chiyembekezo.+