Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:49, 50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Kumbukirani mawu amene* munandiuza ine mtumiki wanu,

      Mawu amene mumandipatsa nawo chiyembekezo.*

      50 Izi ndi zimene zimandilimbikitsa ndikakhala pamavuto,+

      Chifukwa mawu anu andithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.

  • Aheberi 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma Khristu anali mwana ndipo ankayangʼanira nyumba ya Mulungu mokhulupirika.+ Ife tikhalabe nyumba ya Mulunguyo+ tikapitiriza kukhala ndi ufulu wa kulankhula komanso kugwira mwamphamvu chiyembekezo chimene timachinyadira mpaka mapeto.

  • 1 Petulo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Aneneri amene analosera za kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu anakusonyezani, anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndiponso mosamala kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena