Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mundipatse ine mtumiki wanu mtima womvera kuti ndiweruze anthu anu+ komanso ndizitha kusiyanitsa zabwino ndi zoipa.+ Ndani angathe kuweruza anthu anu ambirimbiriwa?”*

  • Salimo 94:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi amene amalangiza mitundu ya anthu, sangathe kudzudzula?+

      Iye ndi amene amaphunzitsa anthu kuti akhale ozindikira.+

  • Danieli 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+

      Amachotsa mafumu komanso kuika mafumu,+

      Amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+

  • Afilipi 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirize kukula kwambiri,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena