Salimo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino komanso wolungama.+ Nʼchifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende mʼnjira yoyenera.+ Yesaya 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu amaphunzitsa* munthu mʼnjira yoyenereraMulungu wake amamulangiza.+ Yohane 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinalembedwa mʼMabuku a Aneneri kuti: ‘Onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.
8 Yehova ndi wabwino komanso wolungama.+ Nʼchifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende mʼnjira yoyenera.+
45 Zinalembedwa mʼMabuku a Aneneri kuti: ‘Onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.