Yesaya 48:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+
17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+