Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+

      Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+

  • Salimo 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nʼzosilirika kuposa golide,

      Kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+

      Ndipo nʼzotsekemera kuposa uchi,+ kuposa uchi umene ukukha mʼzisa.

  • Miyambo 24:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino.

      Uchi wochokera pazisa za njuchi umatsekemera.

      14 Mofanana ndi zimenezi, dziwa kuti nzeru ndi zabwino kwa iwe.*+

      Ukazipeza, udzakhala ndi tsogolo labwino

      Ndipo chiyembekezo chako sichidzawonongedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena