Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+

      Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+

  • Salimo 119:129
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 129 Zikumbutso zanu nʼzodabwitsa.

      Nʼchifukwa chake ine ndimazitsatira.

  • Yeremiya 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+

      Mawu anu anakondweretsa komanso kusangalatsa mtima wanga,

      Chifukwa ine ndimatchedwa ndi dzina lanu, inu Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena