-
2 Mbiri 24:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli mʼchipululu. 10 Akalonga onse ndi anthu onse anasangalala,+ ndipo ankabweretsa ndalama za msonkhowo nʼkumaziponya mʼbokosi lija mpaka linadzaza.*
-