Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:105
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,

      Komanso kuwala kounikira njira yanga.+

  • Miyambo 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+

      Ndipo malangizo ndi kuwala,+

      Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+

  • 2 Akorinto 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Popeza Mulungu ndi amene anati: “Kuwale kuchokera mumdima,”+ ndipo pogwiritsa ntchito nkhope ya Khristu waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudza kudziwa Mulungu.

  • 2 Petulo 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nʼchifukwa chake sitikayikira ngakhale pangʼono kuti mawu aulosiwa adzakwaniritsidwa ndipo mukuchita bwino kuwaganizira mozama. Mawu amenewa aziwala mʼmitima yanu ngati nyale+ imene ikuwala mumdima. Pitirizani kuchita zimenezi mpaka mʼbandakucha, nthanda*+ itatuluka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena