Salimo 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mofanana ndi mbawala imene imalakalaka mitsinje ya madzi,Inenso* ndikulakalaka inu Mulungu. 1 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma monga ana ongobadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasungunula* umene uli mʼMawu a Mulungu. Mukamamwa mkaka umenewo, ukuthandizani kuti mukule nʼkukhala oyenera chipulumutso.+
2 Koma monga ana ongobadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasungunula* umene uli mʼMawu a Mulungu. Mukamamwa mkaka umenewo, ukuthandizani kuti mukule nʼkukhala oyenera chipulumutso.+