Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu Yehova Mulungu wathu amayankha mapemphero athu nthawi zonse. Kodi pali mtundu winanso wamphamvu umene milungu yake ili nawo pafupi chonchi?+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndi pothawira pathu komanso mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya mavuto.+ Salimo 145:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi onse amene amamuitana,+Onse amene amamuitana mʼchoonadi.*+
7 Pajatu Yehova Mulungu wathu amayankha mapemphero athu nthawi zonse. Kodi pali mtundu winanso wamphamvu umene milungu yake ili nawo pafupi chonchi?+
46 Mulungu ndi pothawira pathu komanso mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya mavuto.+