Salimo 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+Iye amapulumutsa anthu amene akudzimvera chisoni mumtima mwawo.*+ Yakobo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yandikirani Mulungu ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu+ okayikakayika inu.
18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+Iye amapulumutsa anthu amene akudzimvera chisoni mumtima mwawo.*+
8 Yandikirani Mulungu ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu+ okayikakayika inu.