Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakhutira* ndi gawo labwino komanso losangalatsa kwambiri,*Choncho milomo yanga idzakutamandani pofuula mosangalala.+ Salimo 71:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ndili mnyamata,+Ndipo mpaka pano ndikupitiriza kulengeza ntchito zanu zodabwitsa.+ Salimo 145:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo azidzalankhula mosangalala akadzakumbukira ubwino wanu wochuluka,+Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa cha chilungamo chanu.+
5 Ndakhutira* ndi gawo labwino komanso losangalatsa kwambiri,*Choncho milomo yanga idzakutamandani pofuula mosangalala.+
17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ndili mnyamata,+Ndipo mpaka pano ndikupitiriza kulengeza ntchito zanu zodabwitsa.+
7 Iwo azidzalankhula mosangalala akadzakumbukira ubwino wanu wochuluka,+Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa cha chilungamo chanu.+