16 Anthu amene ali ndi vuto losaona ndidzawatsogolera kuti ayende mʼnjira imene sakuidziwa.+
Ndidzawadutsitsa mʼnjira zachilendo.+
Mdima ndidzausandutsa kuwala pamaso pawo+
Ndipo malo okumbikakumbika ndidzawasalaza.+
Zimenezi ndi zimene ndidzawachitire ndipo sindidzawasiya.”