Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 112:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Kwa anthu owongoka mtima iye amawala ngati kuwala kumene kumaunika mumdima.+

      ח [Heth]

      Iye ndi wokoma mtima,* wachifundo+ komanso wolungama.

  • Miyambo 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma njira ya olungama ili ngati kuwala kwamphamvu kwa mʼmawa

      Kumene kumawonjezereka mpaka kunja kutawala kwambiri.+

  • Yesaya 30:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kuwala kwa mwezi wathunthu kudzakhala ngati kuwala kwa dzuwa. Ndipo kuwala kwa dzuwa kudzakhala kwamphamvu kwambiri kuwonjezeka maulendo 7,+ ngati kuwala kwa masiku 7. Zimenezi zidzachitika pa tsiku limene Yehova adzamange mabala* a anthu ake+ amene anavulala ndi kuchiritsa mabala aakulu amene anavulala pamene ankawalanga.+

  • Mika 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ndidzapirira mkwiyo wa Yehova,

      Chifukwa ndamuchimwira.+

      Ndidzaupirira mpaka ataweruza mlandu wanga nʼkundichitira chilungamo.

      Iye adzandipititsa pamalo owala,

      Ndipo ndidzaona chilungamo chake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena